Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 60 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿قَالَ ٱلۡمَلَأُ مِن قَوۡمِهِۦٓ إِنَّا لَنَرَىٰكَ فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٖ ﴾
[الأعرَاف: 60]
﴿قال الملأ من قومه إنا لنراك في ضلال مبين﴾ [الأعرَاف: 60]
Khaled Ibrahim Betala “Akuluakulu a mwa anthu ake adati: “Ndithu ife tikukuona kuti uli m’kusokera koonekera (potiletsa izi zomwe tidawapeza nazo makolo athu).” |