×

“Ndipo musakhale mu msewu uliwonse ndi kumaopseza anthu okhulupirira ndi kuwaletsa kutsatira 7:86 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:86) ayat 86 in Chichewa

7:86 Surah Al-A‘raf ayat 86 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 86 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿وَلَا تَقۡعُدُواْ بِكُلِّ صِرَٰطٖ تُوعِدُونَ وَتَصُدُّونَ عَن سَبِيلِ ٱللَّهِ مَنۡ ءَامَنَ بِهِۦ وَتَبۡغُونَهَا عِوَجٗاۚ وَٱذۡكُرُوٓاْ إِذۡ كُنتُمۡ قَلِيلٗا فَكَثَّرَكُمۡۖ وَٱنظُرُواْ كَيۡفَ كَانَ عَٰقِبَةُ ٱلۡمُفۡسِدِينَ ﴾
[الأعرَاف: 86]

“Ndipo musakhale mu msewu uliwonse ndi kumaopseza anthu okhulupirira ndi kuwaletsa kutsatira njira ya Mulungu ndi kufunafuna njira yoti mukhotetsere njirayo. Kumbukirani mmene adakuchulukitsirani inu pamene mudali ochepa. Ndipo onani mmene adalili mapeto a anthu ochita zoipa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تقعدوا بكل صراط توعدون وتصدون عن سبيل الله من آمن به, باللغة نيانجا

﴿ولا تقعدوا بكل صراط توعدون وتصدون عن سبيل الله من آمن به﴾ [الأعرَاف: 86]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo musamawakhalire anthu pa njira iliyonse mowabisalira ndi kumawaopseza, ndi kuwatsekereza kuyenda pa njira ya Allah amene amkhulupirira Iye, ndi kufuna kuikhotetsa njirayo (kuti anthu asaitsate). Ndipo kumbukirani pamene mudali ochepa nakuchulukitsani. Ndipo onani momwe adalili mapeto a owononga.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek