Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 88 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿۞ قَالَ ٱلۡمَلَأُ ٱلَّذِينَ ٱسۡتَكۡبَرُواْ مِن قَوۡمِهِۦ لَنُخۡرِجَنَّكَ يَٰشُعَيۡبُ وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ مَعَكَ مِن قَرۡيَتِنَآ أَوۡ لَتَعُودُنَّ فِي مِلَّتِنَاۚ قَالَ أَوَلَوۡ كُنَّا كَٰرِهِينَ ﴾
[الأعرَاف: 88]
﴿قال الملأ الذين استكبروا من قومه لنخرجنك ياشعيب والذين آمنوا معك من﴾ [الأعرَاف: 88]
Khaled Ibrahim Betala “۞ Akuluakulu omwe adadzikuza mwa anthu ake, adanena: “Tikupirikitsa, iwe Shuaib m’mudzi mwathu muno ndi amene akhulupirira pamodzi nawe, pokhapokha mutabwerera ku chipembedzo chathu.” (Iye) adati: “Kodi ngakhale kuti tikuchida?” |