×

Ndipo mafumu a iwo amene sadakhulupirire a mtundu wa Shaibu adati: “Ngati 7:90 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:90) ayat 90 in Chichewa

7:90 Surah Al-A‘raf ayat 90 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 90 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿وَقَالَ ٱلۡمَلَأُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ مِن قَوۡمِهِۦ لَئِنِ ٱتَّبَعۡتُمۡ شُعَيۡبًا إِنَّكُمۡ إِذٗا لَّخَٰسِرُونَ ﴾
[الأعرَاف: 90]

Ndipo mafumu a iwo amene sadakhulupirire a mtundu wa Shaibu adati: “Ngati inu mutsatira Shaibu ndithudi, mudzakhala olephera pa zochita zanu.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الملأ الذين كفروا من قومه لئن اتبعتم شعيبا إنكم إذا لخاسرون, باللغة نيانجا

﴿وقال الملأ الذين كفروا من قومه لئن اتبعتم شعيبا إنكم إذا لخاسرون﴾ [الأعرَاف: 90]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akuluakulu mwa anthu ake omwe sadakhulupirire adati: “Ngati mutsatira Shuaib ndithudi pamenepo ndiye kuti mukhala otayika.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek