Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma‘arij ayat 11 - المَعَارج - Page - Juz 29
﴿يُبَصَّرُونَهُمۡۚ يَوَدُّ ٱلۡمُجۡرِمُ لَوۡ يَفۡتَدِي مِنۡ عَذَابِ يَوۡمِئِذِۭ بِبَنِيهِ ﴾
[المَعَارج: 11]
﴿يبصرونهم يود المجرم لو يفتدي من عذاب يومئذ ببنيه﴾ [المَعَارج: 11]
Khaled Ibrahim Betala “Ngakhale adzawalole kuti aonane ndi kudziwana pakati pawo (sadzafunsana). Wochimwa adzalakalaka kuti akadaziwombola ku chilango cha tsiku limenelo ndi ana ake |