Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma‘arij ayat 39 - المَعَارج - Page - Juz 29
﴿كـَلَّآۖ إِنَّا خَلَقۡنَٰهُم مِّمَّا يَعۡلَمُونَ ﴾
[المَعَارج: 39]
﴿كلا إنا خلقناهم مما يعلمون﴾ [المَعَارج: 39]
Khaled Ibrahim Betala “Asiye (kukhumba kwawo kokalowa ku Munda wamtendere)! Ndithu Ife tidawalenga kuchokera m’zimene akudziwa (madzi opanda pake) |