Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 1 - الجِن - Page - Juz 29
﴿قُلۡ أُوحِيَ إِلَيَّ أَنَّهُ ٱسۡتَمَعَ نَفَرٞ مِّنَ ٱلۡجِنِّ فَقَالُوٓاْ إِنَّا سَمِعۡنَا قُرۡءَانًا عَجَبٗا ﴾
[الجِن: 1]
﴿قل أوحي إلي أنه استمع نفر من الجن فقالوا إنا سمعنا قرآنا﴾ [الجِن: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Nena (iwe Mtumiki (s.a.w), kwa anthu ako): “Kwavumbulutsidwa kwa ine kuti gulu la ziwanda lidamvetsera (kuwerenga kwanga kwa Qur’an) ndipo lidanena (kumtundu wawo): ndithu tamvetsera Qur’an yodabwitsa (ikuwerengedwa) |