Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 12 - الجِن - Page - Juz 29
﴿وَأَنَّا ظَنَنَّآ أَن لَّن نُّعۡجِزَ ٱللَّهَ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَلَن نُّعۡجِزَهُۥ هَرَبٗا ﴾
[الجِن: 12]
﴿وأنا ظننا أن لن نعجز الله في الأرض ولن نعجزه هربا﴾ [الجِن: 12]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu ife tidadziwa kuti Allah sitingathe kumlepheretsa (lamulo Lake pa ife paliponse tingakhale) pa dziko lapansi, ndipo sitingamlepheretsenso pomzemba ndi kuthawira (kumwamba) |