Quran with Chichewa translation - Surah Al-Muzzammil ayat 19 - المُزمل - Page - Juz 29
﴿إِنَّ هَٰذِهِۦ تَذۡكِرَةٞۖ فَمَن شَآءَ ٱتَّخَذَ إِلَىٰ رَبِّهِۦ سَبِيلًا ﴾
[المُزمل: 19]
﴿إن هذه تذكرة فمن شاء اتخذ إلى ربه سبيلا﴾ [المُزمل: 19]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithudi, ma Ayah awa (amene akunena za kuwopsa kwa Qiyâma) ndichikumbutso. Choncho amene akufuna (kuthandizika nawo) ayende panjira ya Mbuye wake (pokwaniritsa malamulo Ake ndi kuleka zoipa) |