Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mursalat ayat 38 - المُرسَلات - Page - Juz 29
﴿هَٰذَا يَوۡمُ ٱلۡفَصۡلِۖ جَمَعۡنَٰكُمۡ وَٱلۡأَوَّلِينَ ﴾
[المُرسَلات: 38]
﴿هذا يوم الفصل جمعناكم والأولين﴾ [المُرسَلات: 38]
Khaled Ibrahim Betala “(Adzauzidwa kuti): Ili ndi tsiku loweruza (pakati pa abwino ndi oipa takusonkhanitsani inu (otsutsa Muhammad {s.a.w}), ndi akale (otsutsa aneneri akale) |