×

Ngati iwe uwapambana pomenyana nawo nkhondo, alange kwambiri kuti ukhoza kuthamangitsa iwo 8:57 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:57) ayat 57 in Chichewa

8:57 Surah Al-Anfal ayat 57 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 57 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿فَإِمَّا تَثۡقَفَنَّهُمۡ فِي ٱلۡحَرۡبِ فَشَرِّدۡ بِهِم مَّنۡ خَلۡفَهُمۡ لَعَلَّهُمۡ يَذَّكَّرُونَ ﴾
[الأنفَال: 57]

Ngati iwe uwapambana pomenyana nawo nkhondo, alange kwambiri kuti ukhoza kuthamangitsa iwo amene ali kumbuyo kwawo kuti akhoza kuphunzira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإما تثقفنهم في الحرب فشرد بهم من خلفهم لعلهم يذكرون, باللغة نيانجا

﴿فإما تثقفنهم في الحرب فشرد بهم من خلفهم لعلهم يذكرون﴾ [الأنفَال: 57]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho, ngati uwapeza ku nkhondo, (menyana nawo), uwabalalitse (kuti likhale phunziro kwa) amene ali pambuyo pawo kuti iwo azindikire
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek