Quran with Chichewa translation - Surah AT-Tariq ayat 4 - الطَّارق - Page - Juz 30
﴿إِن كُلُّ نَفۡسٖ لَّمَّا عَلَيۡهَا حَافِظٞ ﴾
[الطَّارق: 4]
﴿إن كل نفس لما عليها حافظ﴾ [الطَّارق: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithudi palibe mzimu uliwonse koma uli ndi msungi wake (amene akuuyang’anira ndikulemba zonse zochita zake) |