×

Ena alipo amene avomera zoipa zawo, iwo asakaniza ntchito zawo zabwino ndi 9:102 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:102) ayat 102 in Chichewa

9:102 Surah At-Taubah ayat 102 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 102 - التوبَة - Page - Juz 11

﴿وَءَاخَرُونَ ٱعۡتَرَفُواْ بِذُنُوبِهِمۡ خَلَطُواْ عَمَلٗا صَٰلِحٗا وَءَاخَرَ سَيِّئًا عَسَى ٱللَّهُ أَن يَتُوبَ عَلَيۡهِمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ غَفُورٞ رَّحِيمٌ ﴾
[التوبَة: 102]

Ena alipo amene avomera zoipa zawo, iwo asakaniza ntchito zawo zabwino ndi ntchito zawo zoipa. Mwina Mulungu adzawalandira kulapa kwawo. Ndithudi Mulungu ndi wokhululukira ndi Mwini chisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وآخرون اعترفوا بذنوبهم خلطوا عملا صالحا وآخر سيئا عسى الله أن يتوب, باللغة نيانجا

﴿وآخرون اعترفوا بذنوبهم خلطوا عملا صالحا وآخر سيئا عسى الله أن يتوب﴾ [التوبَة: 102]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo alipo ena omwe avomereza uchimo wawo (nalapa kwa Allah). Asakaniza zochita zabwino ndi zina zoipa. Ndithu Allah alandira kulapa kwawo. Ndithu Allah Ngokhululuka, Ngwachisoni chosatha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek