×

Sizili zoyenera kwa Mtumwi ndi anthu okhulupirira kuwapemphera chikhululukiro anthu opembedza mafano 9:113 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:113) ayat 113 in Chichewa

9:113 Surah At-Taubah ayat 113 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 113 - التوبَة - Page - Juz 11

﴿مَا كَانَ لِلنَّبِيِّ وَٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ أَن يَسۡتَغۡفِرُواْ لِلۡمُشۡرِكِينَ وَلَوۡ كَانُوٓاْ أُوْلِي قُرۡبَىٰ مِنۢ بَعۡدِ مَا تَبَيَّنَ لَهُمۡ أَنَّهُمۡ أَصۡحَٰبُ ٱلۡجَحِيمِ ﴾
[التوبَة: 113]

Sizili zoyenera kwa Mtumwi ndi anthu okhulupirira kuwapemphera chikhululukiro anthu opembedza mafano ngakhale kuti iwo ndi a chibale awo pambuyo podziwika kwa iwo kuti iwo ndi anthu a kumoto

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما كان للنبي والذين آمنوا أن يستغفروا للمشركين ولو كانوا أولي قربى, باللغة نيانجا

﴿ما كان للنبي والذين آمنوا أن يستغفروا للمشركين ولو كانوا أولي قربى﴾ [التوبَة: 113]

Khaled Ibrahim Betala
“Nkosayenera kwa Mneneri ndi amene akhulupirira kuwapemphera chikhululuko opembedza mafano ngakhale atakhala abale awo, pambuyo poonekera kwa iwo kuti iwowo ndi anthu a ku Moto
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek