×

Ndipo iwo sapereka chopereka chochepa kapena chochuluka kapena kudutsa dambo lililonse koma 9:121 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:121) ayat 121 in Chichewa

9:121 Surah At-Taubah ayat 121 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 121 - التوبَة - Page - Juz 11

﴿وَلَا يُنفِقُونَ نَفَقَةٗ صَغِيرَةٗ وَلَا كَبِيرَةٗ وَلَا يَقۡطَعُونَ وَادِيًا إِلَّا كُتِبَ لَهُمۡ لِيَجۡزِيَهُمُ ٱللَّهُ أَحۡسَنَ مَا كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[التوبَة: 121]

Ndipo iwo sapereka chopereka chochepa kapena chochuluka kapena kudutsa dambo lililonse koma kuti zidalembedwa ngati mphotho zabwino kwa iwo ndi kuti Mulungu adzawalipire zabwino zimene ankachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا ينفقون نفقة صغيرة ولا كبيرة ولا يقطعون واديا إلا كتب لهم, باللغة نيانجا

﴿ولا ينفقون نفقة صغيرة ولا كبيرة ولا يقطعون واديا إلا كتب لهم﴾ [التوبَة: 121]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo sangapereke chopereka chaching’ono kapena chachikulu, ndipo sangadutse ntunda wachigwa; koma kulembedwa kwa iwo kuti Allah adzawalipira malipiro abwino pa zomwe adali kuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek