×

Pitani kunkhondo kaya muli opepukidwa kapena olemedwa. Limbikirani kwambiri ndi chuma chanu 9:41 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:41) ayat 41 in Chichewa

9:41 Surah At-Taubah ayat 41 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 41 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿ٱنفِرُواْ خِفَافٗا وَثِقَالٗا وَجَٰهِدُواْ بِأَمۡوَٰلِكُمۡ وَأَنفُسِكُمۡ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِۚ ذَٰلِكُمۡ خَيۡرٞ لَّكُمۡ إِن كُنتُمۡ تَعۡلَمُونَ ﴾
[التوبَة: 41]

Pitani kunkhondo kaya muli opepukidwa kapena olemedwa. Limbikirani kwambiri ndi chuma chanu pamodzi ndi inu nomwe m’njira ya Mulungu. Ichi ndi chinthu chabwino kwa inu ngati mukadadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: انفروا خفافا وثقالا وجاهدوا بأموالكم وأنفسكم في سبيل الله ذلكم خير لكم, باللغة نيانجا

﴿انفروا خفافا وثقالا وجاهدوا بأموالكم وأنفسكم في سبيل الله ذلكم خير لكم﴾ [التوبَة: 41]

Khaled Ibrahim Betala
“Pitani (mukamenyane) muli opepukidwa ndi olemedwa; ndipo menyerani njira ya Allah nchuma chanu ndi inu nomwe. Zimenezi nzabwino kwa inu ngati muli anthu odziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek