×

Mulungu akukhululukire iwe: Kodi ndi chifukwa chiyani unawapatsa chilolezo mpaka pamene iwo 9:43 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:43) ayat 43 in Chichewa

9:43 Surah At-Taubah ayat 43 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 43 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿عَفَا ٱللَّهُ عَنكَ لِمَ أَذِنتَ لَهُمۡ حَتَّىٰ يَتَبَيَّنَ لَكَ ٱلَّذِينَ صَدَقُواْ وَتَعۡلَمَ ٱلۡكَٰذِبِينَ ﴾
[التوبَة: 43]

Mulungu akukhululukire iwe: Kodi ndi chifukwa chiyani unawapatsa chilolezo mpaka pamene iwo onena zoona anaoneka kwa iwe poyera ndi kuwadziwa onama

❮ Previous Next ❯

ترجمة: عفا الله عنك لم أذنت لهم حتى يتبين لك الذين صدقوا وتعلم, باللغة نيانجا

﴿عفا الله عنك لم أذنت لهم حتى يتبين لك الذين صدقوا وتعلم﴾ [التوبَة: 43]

Khaled Ibrahim Betala
Allah wakukhululukira. Bwanji wawaloleza kutsalira? (Ukadayembekeza) kufikira adziwike kwa iwe amene akunena zoona, ndikuti uwadziwe abodza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek