×

Mulungu walonjeza anthu a chinyengo, amuna ndi akazi ndiponso anthu osakhulupirira moto 9:68 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:68) ayat 68 in Chichewa

9:68 Surah At-Taubah ayat 68 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 68 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿وَعَدَ ٱللَّهُ ٱلۡمُنَٰفِقِينَ وَٱلۡمُنَٰفِقَٰتِ وَٱلۡكُفَّارَ نَارَ جَهَنَّمَ خَٰلِدِينَ فِيهَاۚ هِيَ حَسۡبُهُمۡۚ وَلَعَنَهُمُ ٱللَّهُۖ وَلَهُمۡ عَذَابٞ مُّقِيمٞ ﴾
[التوبَة: 68]

Mulungu walonjeza anthu a chinyengo, amuna ndi akazi ndiponso anthu osakhulupirira moto wa ku Gahena ndipo iwo adzakhala kumeneko mpaka kalekale. Chimenechi ndi chilango chowayeneradi. Mulungu wawatemberera ndipo chawo chidzakhala chilango chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وعد الله المنافقين والمنافقات والكفار نار جهنم خالدين فيها هي حسبهم ولعنهم, باللغة نيانجا

﴿وعد الله المنافقين والمنافقات والكفار نار جهنم خالدين فيها هي حسبهم ولعنهم﴾ [التوبَة: 68]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah walonjeza achiphamaso aamuna ndi achiphamaso aakazi ndi akafiri moto wa Jahannam, akakhala m’menemo nthawi yaitali. Umenewo ukukwanira kwa iwo (kuwalanga). Ndipo Allah wawatembelera, ndipo iwo adzapeza chilango cha nthawi zonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek