Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 106 - هُود - Page - Juz 12
﴿فَأَمَّا ٱلَّذِينَ شَقُواْ فَفِي ٱلنَّارِ لَهُمۡ فِيهَا زَفِيرٞ وَشَهِيقٌ ﴾
[هُود: 106]
﴿فأما الذين شقوا ففي النار لهم فيها زفير وشهيق﴾ [هُود: 106]
Khaled Ibrahim Betala “Tsono amene adzakhala oipa kobwerera kwawo nkumoto. Iwo adzakhala m’menemo akufuula potulutsa mawu ndi kuwabweza (monga kulira kwa bulu) |