×

Iwo adzakhala komweko mpaka pamene kumwamba ndi dziko lapansi zidzakhale zilipobe kupatula 11:107 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Hud ⮕ (11:107) ayat 107 in Chichewa

11:107 Surah Hud ayat 107 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 107 - هُود - Page - Juz 12

﴿خَٰلِدِينَ فِيهَا مَا دَامَتِ ٱلسَّمَٰوَٰتُ وَٱلۡأَرۡضُ إِلَّا مَا شَآءَ رَبُّكَۚ إِنَّ رَبَّكَ فَعَّالٞ لِّمَا يُرِيدُ ﴾
[هُود: 107]

Iwo adzakhala komweko mpaka pamene kumwamba ndi dziko lapansi zidzakhale zilipobe kupatula ngati Ambuye wako afuna kusintha. Ndithudi Ambuye wako amachita zimene afuna

❮ Previous Next ❯

ترجمة: خالدين فيها ما دامت السموات والأرض إلا ما شاء ربك إن ربك, باللغة نيانجا

﴿خالدين فيها ما دامت السموات والأرض إلا ما شاء ربك إن ربك﴾ [هُود: 107]

Khaled Ibrahim Betala
“Adzakhala m’menemo nthawi yaitali momwe thambo ndi nthaka zidzakhalire, kupatula Mbuye wako akadzafuna. Ndithu Mbuye wako Ngochita chimene wafuna
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek