Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 39 - يُوسُف - Page - Juz 12
﴿يَٰصَٰحِبَيِ ٱلسِّجۡنِ ءَأَرۡبَابٞ مُّتَفَرِّقُونَ خَيۡرٌ أَمِ ٱللَّهُ ٱلۡوَٰحِدُ ٱلۡقَهَّارُ ﴾
[يُوسُف: 39]
﴿ياصاحبي السجن أأرباب متفرقون خير أم الله الواحد القهار﴾ [يُوسُف: 39]
Khaled Ibrahim Betala ““E inu anzanga awiri a m’ndende! Kodi milungu yambiri yosiyana ndiyo yabwino (kupembedzedwa), kapena Allah Mmodzi Mwini mphamvu (pachilichonse)?” |