×

Yakobo adati, “Iyayi! Mizimu yanu yakunyengani kuchita zoipa. Koma kupirira ndi kwabwino. 12:83 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:83) ayat 83 in Chichewa

12:83 Surah Yusuf ayat 83 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 83 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿قَالَ بَلۡ سَوَّلَتۡ لَكُمۡ أَنفُسُكُمۡ أَمۡرٗاۖ فَصَبۡرٞ جَمِيلٌۖ عَسَى ٱللَّهُ أَن يَأۡتِيَنِي بِهِمۡ جَمِيعًاۚ إِنَّهُۥ هُوَ ٱلۡعَلِيمُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[يُوسُف: 83]

Yakobo adati, “Iyayi! Mizimu yanu yakunyengani kuchita zoipa. Koma kupirira ndi kwabwino. Mwina Mulungu adzawabweretsa onse awiri kwa ine. Ndithudi Iye yekha amadziwa zinthu zonse ndiponso ndi waluntha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال بل سولت لكم أنفسكم أمرا فصبر جميل عسى الله أن يأتيني, باللغة نيانجا

﴿قال بل سولت لكم أنفسكم أمرا فصبر جميل عسى الله أن يأتيني﴾ [يُوسُف: 83]

Khaled Ibrahim Betala
“(Ya’qub) adati: “Koma mitima yanu yakukometserani chinthu. (Kwanga ndi) kupirira kwabwino kokha basi. Mwina Allah adzandibweretsera onse pamodzi. Ndithudi, Iye Ngodziwa, Ngwanzeru zakuya.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek