Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 57 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿وَيَجۡعَلُونَ لِلَّهِ ٱلۡبَنَٰتِ سُبۡحَٰنَهُۥ وَلَهُم مَّا يَشۡتَهُونَ ﴾
[النَّحل: 57]
﴿ويجعلون لله البنات سبحانه ولهم ما يشتهون﴾ [النَّحل: 57]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (mwaumbuli) akumuikira Allah ana aakazi (ponena kuti adabereka ana aakazi) Subuhana! (Wayera Allah kuzimenezi!) Ndipo iwo (eni) amadzifunira amene amawakonda (omwe ndi ana achimuna) |