Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 129 - طه - Page - Juz 16
﴿وَلَوۡلَا كَلِمَةٞ سَبَقَتۡ مِن رَّبِّكَ لَكَانَ لِزَامٗا وَأَجَلٞ مُّسَمّٗى ﴾
[طه: 129]
﴿ولولا كلمة سبقت من ربك لكان لزاما وأجل مسمى﴾ [طه: 129]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo pakadapanda liwu lomwe lidatsogola kuchokera kwa Mbuye wako (lochedwetsera chilango) ndi nthawi yomwe idaikidwa, ndithu (chilango) chikadawafika (tsopano lomwe lino) |