Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 133 - طه - Page - Juz 16
﴿وَقَالُواْ لَوۡلَا يَأۡتِينَا بِـَٔايَةٖ مِّن رَّبِّهِۦٓۚ أَوَلَمۡ تَأۡتِهِم بَيِّنَةُ مَا فِي ٱلصُّحُفِ ٱلۡأُولَىٰ ﴾
[طه: 133]
﴿وقالوا لولا يأتينا بآية من ربه أو لم تأتهم بينة ما في﴾ [طه: 133]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (osakhulupirira) adanena: “Chifukwa ninji sakutibweretsera chizizwa kuchokera kwa Mbuye wake?” Kodi sudawafike umboni woonekera wa zomwe zili m’mabuku akale? (Kodi sadakhutitsidwe ndi Qur’an chomwe ndi chizizwa chachikulu).” |