Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 55 - الحج - Page - Juz 17
﴿وَلَا يَزَالُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ فِي مِرۡيَةٖ مِّنۡهُ حَتَّىٰ تَأۡتِيَهُمُ ٱلسَّاعَةُ بَغۡتَةً أَوۡ يَأۡتِيَهُمۡ عَذَابُ يَوۡمٍ عَقِيمٍ ﴾
[الحج: 55]
﴿ولا يزال الذين كفروا في مرية منه حتى تأتيهم الساعة بغتة أو﴾ [الحج: 55]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene sadakhulupirire apitilira kukhala m’chikaiko ndi chimenecho (wadza nachocho) kufikira tsiku la chimaliziro liwadzera mowatutumutsa, kapena chiwadzera chilango pa tsiku lopanda chabwino (kwa iwo) |