Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 38 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿إِنۡ هُوَ إِلَّا رَجُلٌ ٱفۡتَرَىٰ عَلَى ٱللَّهِ كَذِبٗا وَمَا نَحۡنُ لَهُۥ بِمُؤۡمِنِينَ ﴾
[المؤمنُون: 38]
﴿إن هو إلا رجل افترى على الله كذبا وما نحن له بمؤمنين﴾ [المؤمنُون: 38]
Khaled Ibrahim Betala “Uyu saali kanthu (amene akudzitcha kuti ndi Mtumiki) koma ndi munthu basi, akupekera Allah bodza, ndipo ife sitimkhulupirira.” |