×

Pakadakhala popanda chisomo cha Mulungu kwa inu, nonse mukanaonongedwa. Ndithudi Mulungu ndi 24:20 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:20) ayat 20 in Chichewa

24:20 Surah An-Nur ayat 20 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 20 - النور - Page - Juz 18

﴿وَلَوۡلَا فَضۡلُ ٱللَّهِ عَلَيۡكُمۡ وَرَحۡمَتُهُۥ وَأَنَّ ٱللَّهَ رَءُوفٞ رَّحِيمٞ ﴾
[النور: 20]

Pakadakhala popanda chisomo cha Mulungu kwa inu, nonse mukanaonongedwa. Ndithudi Mulungu ndi wabwino ndiponso wachisoni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولولا فضل الله عليكم ورحمته وأن الله رءوف رحيم, باللغة نيانجا

﴿ولولا فضل الله عليكم ورحمته وأن الله رءوف رحيم﴾ [النور: 20]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pakadapanda ubwino wa Allah ndi chifundo Chake pa inu, (pakadapezeka zauve). Koma ndithu Allah Ngoleza; Ngwachisoni chosatha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek