×

Auze amuna okhulupirira kuti azitsitsa maso awo ndi kulewa chigololo. Zimenezi ndizo 24:30 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:30) ayat 30 in Chichewa

24:30 Surah An-Nur ayat 30 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 30 - النور - Page - Juz 18

﴿قُل لِّلۡمُؤۡمِنِينَ يَغُضُّواْ مِنۡ أَبۡصَٰرِهِمۡ وَيَحۡفَظُواْ فُرُوجَهُمۡۚ ذَٰلِكَ أَزۡكَىٰ لَهُمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ خَبِيرُۢ بِمَا يَصۡنَعُونَ ﴾
[النور: 30]

Auze amuna okhulupirira kuti azitsitsa maso awo ndi kulewa chigololo. Zimenezi ndizo zimene zidzayeretsa moyo wawo. Mulungu amadziwa zonse zimene mumachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل للمؤمنين يغضوا من أبصارهم ويحفظوا فروجهم ذلك أزكى لهم إن الله, باللغة نيانجا

﴿قل للمؤمنين يغضوا من أبصارهم ويحفظوا فروجهم ذلك أزكى لهم إن الله﴾ [النور: 30]

Khaled Ibrahim Betala
“Auze okhulupirira achimuna kuti adzolitse maso awo (asayang’ane zoletsedwa), ndipo asunge umaliseche wawo. Ichi nchoyera kwambiri kwa iwo. Ndithu Allah akudziwa nkhani za zonse zomwe achita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek