Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 15 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿قَالَ كـَلَّاۖ فَٱذۡهَبَا بِـَٔايَٰتِنَآۖ إِنَّا مَعَكُم مُّسۡتَمِعُونَ ﴾
[الشعراء: 15]
﴿قال كلا فاذهبا بآياتنا إنا معكم مستمعون﴾ [الشعراء: 15]
Khaled Ibrahim Betala “(Allah) adati: “Iyayi! Pitani pamodzi ndi zozizwa Zathu; ndithu Ife tikakhala nanu limodzi (pokuthangatani) uku tikumvetsera (zimene azikanena).” |