×

Mose adawamwetsera nkhosa zawo ndipo adachoka ndi kukakhala pa m’thunzi nati, “Ambuye, 28:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:24) ayat 24 in Chichewa

28:24 Surah Al-Qasas ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 24 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿فَسَقَىٰ لَهُمَا ثُمَّ تَوَلَّىٰٓ إِلَى ٱلظِّلِّ فَقَالَ رَبِّ إِنِّي لِمَآ أَنزَلۡتَ إِلَيَّ مِنۡ خَيۡرٖ فَقِيرٞ ﴾
[القَصَص: 24]

Mose adawamwetsera nkhosa zawo ndipo adachoka ndi kukakhala pa m’thunzi nati, “Ambuye, ine ndili kusowa zabwino zimene munganditumize.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فسقى لهما ثم تولى إلى الظل فقال رب إني لما أنـزلت إلي, باللغة نيانجا

﴿فسقى لهما ثم تولى إلى الظل فقال رب إني لما أنـزلت إلي﴾ [القَصَص: 24]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho (Mûsa) adawamwetsera (ziweto zawo); kenako adapita pamthunzi, ndipo adati: “E Mbuye wanga! Ndithu ine ndiwosaukira chabwino chimene munditsitsire.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek