Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 9 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿وَقَالَتِ ٱمۡرَأَتُ فِرۡعَوۡنَ قُرَّتُ عَيۡنٖ لِّي وَلَكَۖ لَا تَقۡتُلُوهُ عَسَىٰٓ أَن يَنفَعَنَآ أَوۡ نَتَّخِذَهُۥ وَلَدٗا وَهُمۡ لَا يَشۡعُرُونَ ﴾
[القَصَص: 9]
﴿وقالت امرأة فرعون قرة عين لي ولك لا تقتلوه عسى أن ينفعنا﴾ [القَصَص: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo mkazi wa Farawo adati: “(Musamuphe, akhale) chosangalatsa diso langa ndi lako; musamuphe mwina angatithandize, kapena tingam’chite kukhala mwana (wathu.” Adanena izi) iwo asakudziwa (kuti adzakhala m’dani wawo) |