Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 19 - يسٓ - Page - Juz 22
﴿قَالُواْ طَٰٓئِرُكُم مَّعَكُمۡ أَئِن ذُكِّرۡتُمۚ بَلۡ أَنتُمۡ قَوۡمٞ مُّسۡرِفُونَ ﴾
[يسٓ: 19]
﴿قالوا طائركم معكم أإن ذكرتم بل أنتم قوم مسرفون﴾ [يسٓ: 19]
Khaled Ibrahim Betala “(Atumiki) adati: “Tsoka lanu lili ndi inu (chifukwa cha kukana kwanu ndi kupitiriza kupembedza mafano). Kodi mukakumbutsidwa (ndi mawu omwe m’kati mwake muli mtendere wanu mukuti takudzetserani masoka; ndi kumatiopseza ndi chilango chowawa)? Koma inu ndi anthu olumpha malire.” |