Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 29 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿إِن كَانَتۡ إِلَّا صَيۡحَةٗ وَٰحِدَةٗ فَإِذَا هُمۡ خَٰمِدُونَ ﴾
[يسٓ: 29]
﴿إن كانت إلا صيحة واحدة فإذا هم خامدون﴾ [يسٓ: 29]
Khaled Ibrahim Betala “(Kuonongeka kwawo) kudali mkuwe umodzi, ndipo nthawi yomweyo adali akufa (izi zidachitika pamene mngelo Gabuliyele adawakuwira mkuwe wamphamvu) |