Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 53 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿إِن كَانَتۡ إِلَّا صَيۡحَةٗ وَٰحِدَةٗ فَإِذَا هُمۡ جَمِيعٞ لَّدَيۡنَا مُحۡضَرُونَ ﴾ 
[يسٓ: 53]
﴿إن كانت إلا صيحة واحدة فإذا هم جميع لدينا محضرون﴾ [يسٓ: 53]
| Khaled Ibrahim Betala “Sipadzakhala (china) koma mkuwe umodzi basi; adzangozindikira iwo onse atabweretsedwa patsogolo Pathu |