×

Koma iwo amene aopa Ambuye wawo ali ndi nyumba zokongola ndi zosanjikizana 39:20 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:20) ayat 20 in Chichewa

39:20 Surah Az-Zumar ayat 20 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 20 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿لَٰكِنِ ٱلَّذِينَ ٱتَّقَوۡاْ رَبَّهُمۡ لَهُمۡ غُرَفٞ مِّن فَوۡقِهَا غُرَفٞ مَّبۡنِيَّةٞ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُۖ وَعۡدَ ٱللَّهِ لَا يُخۡلِفُ ٱللَّهُ ٱلۡمِيعَادَ ﴾
[الزُّمَر: 20]

Koma iwo amene aopa Ambuye wawo ali ndi nyumba zokongola ndi zosanjikizana zimene zamangidwa ndipo pansi pake pamayenda mitsinje. Limeneli ndilo lonjezo la Mulungu ndipo Iye saphwanya lonjezo lake

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لكن الذين اتقوا ربهم لهم غرف من فوقها غرف مبنية تجري من, باللغة نيانجا

﴿لكن الذين اتقوا ربهم لهم غرف من فوقها غرف مبنية تجري من﴾ [الزُّمَر: 20]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma amene aopa Mbuye wawo, iwo adzakhala nazo Nyumba zikuluzikulu zimene zamangidwa mosanjikizana, mitsinje ikuyenda pansi pake. Ili ndi lonjezo lochokera kwa Allah. Allah saphwanya lonjezo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek