Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 27 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿وَقَالَ مُوسَىٰٓ إِنِّي عُذۡتُ بِرَبِّي وَرَبِّكُم مِّن كُلِّ مُتَكَبِّرٖ لَّا يُؤۡمِنُ بِيَوۡمِ ٱلۡحِسَابِ ﴾
[غَافِر: 27]
﴿وقال موسى إني عذت بربي وربكم من كل متكبر لا يؤمن بيوم﴾ [غَافِر: 27]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Mûsa adati (kwa Farawo pa modzi ndi anthu ake): “Ine ndadzitchinjiriza ndi Mbuye wanga amenenso ali Mbuye wanu (ku chiwembu) chochokera kwa aliyense wodzikweza, wosakhulupirira za tsiku la chiwerengero |