Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 42 - الشُّوري - Page - Juz 25
﴿إِنَّمَا ٱلسَّبِيلُ عَلَى ٱلَّذِينَ يَظۡلِمُونَ ٱلنَّاسَ وَيَبۡغُونَ فِي ٱلۡأَرۡضِ بِغَيۡرِ ٱلۡحَقِّۚ أُوْلَٰٓئِكَ لَهُمۡ عَذَابٌ أَلِيمٞ ﴾
[الشُّوري: 42]
﴿إنما السبيل على الذين يظلمون الناس ويبغون في الأرض بغير الحق أولئك﴾ [الشُّوري: 42]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu njira yodzudzulidwira ili kwa amene akupondereza anthu ndi kuchita mtopola pa dziko popanda chifukwa choyenera. Iwowo ndi amene adzalandira chilango chowawa |