Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 43 - الشُّوري - Page - Juz 25
﴿وَلَمَن صَبَرَ وَغَفَرَ إِنَّ ذَٰلِكَ لَمِنۡ عَزۡمِ ٱلۡأُمُورِ ﴾
[الشُّوري: 43]
﴿ولمن صبر وغفر إن ذلك لمن عزم الأمور﴾ [الشُّوري: 43]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene akupirira ndi kukhululuka, (Allah adzamlipira mphoto yaikulu); ndithu kupirirako ndi chimodzi mwa zinthu zazikulu (chofunika kudzilimbikitsa nacho Msilamu pa chikhalidwe chake) |