Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 67 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿ٱلۡأَخِلَّآءُ يَوۡمَئِذِۭ بَعۡضُهُمۡ لِبَعۡضٍ عَدُوٌّ إِلَّا ٱلۡمُتَّقِينَ ﴾
[الزُّخرُف: 67]
﴿الأخلاء يومئذ بعضهم لبعض عدو إلا المتقين﴾ [الزُّخرُف: 67]
Khaled Ibrahim Betala “Abwenzi tsiku limenelo adzakhala odana, wina ndi mnzake, (chifukwa chakuti adali kuthandizana pa zinthu zosalungama ndi zamachimo) kupatula oopa Allah (amene adachita chibwenzi mwa Allah, pothandizana kukwaniritsa malamulo a Allah ndi kusiya zimene Allah waletsa) |