×

Ndipo anthu osakhulupirira amanena zokhudza anthu okhulupirira kuti, “Ngati uthengawu ukadakhala wabwino, 46:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:11) ayat 11 in Chichewa

46:11 Surah Al-Ahqaf ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 11 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ لِلَّذِينَ ءَامَنُواْ لَوۡ كَانَ خَيۡرٗا مَّا سَبَقُونَآ إِلَيۡهِۚ وَإِذۡ لَمۡ يَهۡتَدُواْ بِهِۦ فَسَيَقُولُونَ هَٰذَآ إِفۡكٞ قَدِيمٞ ﴾
[الأحقَاف: 11]

Ndipo anthu osakhulupirira amanena zokhudza anthu okhulupirira kuti, “Ngati uthengawu ukadakhala wabwino, iwo sakadaulandira msanga kuposa ife. Ndipo popeza iwo safuna kuti atsogozedwe ndi uthengawu iwo amati, “Limeneli ndi bodza chabe la anthu akale.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الذين كفروا للذين آمنوا لو كان خيرا ما سبقونا إليه وإذ, باللغة نيانجا

﴿وقال الذين كفروا للذين آمنوا لو كان خيرا ما سبقونا إليه وإذ﴾ [الأحقَاف: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene sadakhulupirire adanena kwa amene adakhulupirira: “(Chipembedzo ichi) chikadakhala chabwino, awa sakadakhala otsogola ku chimenechi pa ife.” Ndipo chifukwa choti sadaongoke nalo (bukuli), akhala akunena: “Ili ndi bodza lakale.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek