×

Awa ndiwo amene tidzalandira zabwino za ntchito zawo ndi kuwakhululukira zoipa zawo. 46:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:16) ayat 16 in Chichewa

46:16 Surah Al-Ahqaf ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 16 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿أُوْلَٰٓئِكَ ٱلَّذِينَ نَتَقَبَّلُ عَنۡهُمۡ أَحۡسَنَ مَا عَمِلُواْ وَنَتَجَاوَزُ عَن سَيِّـَٔاتِهِمۡ فِيٓ أَصۡحَٰبِ ٱلۡجَنَّةِۖ وَعۡدَ ٱلصِّدۡقِ ٱلَّذِي كَانُواْ يُوعَدُونَ ﴾
[الأحقَاف: 16]

Awa ndiwo amene tidzalandira zabwino za ntchito zawo ndi kuwakhululukira zoipa zawo. Iwo adzakhala m’gulu la anthu a ku Paradiso. Lonjezo loona, limene lidalonjezedwa kwa iwo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أولئك الذين نتقبل عنهم أحسن ما عملوا ونتجاوز عن سيئاتهم في أصحاب, باللغة نيانجا

﴿أولئك الذين نتقبل عنهم أحسن ما عملوا ونتجاوز عن سيئاتهم في أصحاب﴾ [الأحقَاف: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Iwowo ndiamene tikuwalandira zabwino zimene adachita ndipo tikuwakhululukira zolakwa zawo. Adzakhala m’gulu la anthu a ku Jannah. Ili ndi lonjezo loona lomwe adalonjezedwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek