×

Ndithudi Mulungu amadziwa zobisika zonse zimene zili mlengalenga ndi padziko lapansi ndipo 49:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hujurat ⮕ (49:18) ayat 18 in Chichewa

49:18 Surah Al-hujurat ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hujurat ayat 18 - الحُجُرَات - Page - Juz 26

﴿إِنَّ ٱللَّهَ يَعۡلَمُ غَيۡبَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ وَٱللَّهُ بَصِيرُۢ بِمَا تَعۡمَلُونَ ﴾
[الحُجُرَات: 18]

Ndithudi Mulungu amadziwa zobisika zonse zimene zili mlengalenga ndi padziko lapansi ndipo Mulungu amaona zonse zimene mumachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله يعلم غيب السموات والأرض والله بصير بما تعملون, باللغة نيانجا

﴿إن الله يعلم غيب السموات والأرض والله بصير بما تعملون﴾ [الحُجُرَات: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Allah akudziwa zobisika za kumwamba ndi za mnthaka. Ndipo Allah akuona zimene mukuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek