×

Akadakhala kuti anthu a m’Buku adakhulupirira ndi kulewa zoipa, Ife tikadawakhululukira machimo 5:65 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:65) ayat 65 in Chichewa

5:65 Surah Al-Ma’idah ayat 65 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 65 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿وَلَوۡ أَنَّ أَهۡلَ ٱلۡكِتَٰبِ ءَامَنُواْ وَٱتَّقَوۡاْ لَكَفَّرۡنَا عَنۡهُمۡ سَيِّـَٔاتِهِمۡ وَلَأَدۡخَلۡنَٰهُمۡ جَنَّٰتِ ٱلنَّعِيمِ ﴾
[المَائدة: 65]

Akadakhala kuti anthu a m’Buku adakhulupirira ndi kulewa zoipa, Ife tikadawakhululukira machimo awo ndi kuwalowetsa m’minda ya mtendere

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو أن أهل الكتاب آمنوا واتقوا لكفرنا عنهم سيئاتهم ولأدخلناهم جنات النعيم, باللغة نيانجا

﴿ولو أن أهل الكتاب آمنوا واتقوا لكفرنا عنهم سيئاتهم ولأدخلناهم جنات النعيم﴾ [المَائدة: 65]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kukadakhala kuti awa anthu a buku adakhulupirira ndi kumuopa Allah, tikadawafafanizira zolakwa zawo, ndi kuwalowetsa m’minda ya mtendere
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek