Quran with Chichewa translation - Surah Adh-Dhariyat ayat 43 - الذَّاريَات - Page - Juz 27
﴿وَفِي ثَمُودَ إِذۡ قِيلَ لَهُمۡ تَمَتَّعُواْ حَتَّىٰ حِينٖ ﴾
[الذَّاريَات: 43]
﴿وفي ثمود إذ قيل لهم تمتعوا حتى حين﴾ [الذَّاريَات: 43]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo m’nkhani ya Samudu (muli chisonyezo) pamene kudanenedwa kwa iwo kuti: “Sangalalani (mnyumba zanu) mpaka nthawi yaikika.” |