Quran with Chichewa translation - Surah AT-Tur ayat 19 - الطُّور - Page - Juz 27
﴿كُلُواْ وَٱشۡرَبُواْ هَنِيٓـَٔۢا بِمَا كُنتُمۡ تَعۡمَلُونَ ﴾
[الطُّور: 19]
﴿كلوا واشربوا هنيئا بما كنتم تعملون﴾ [الطُّور: 19]
Khaled Ibrahim Betala “(Kudzanenedwa kwa iwo): “Idyani (chakudya chamtendere); ndipo imwani mosangalala kukhala malipiro pazimene munkachita (pa dziko lapansi).” |