Quran with Chichewa translation - Surah An-Najm ayat 31 - النَّجم - Page - Juz 27
﴿وَلِلَّهِ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِ لِيَجۡزِيَ ٱلَّذِينَ أَسَٰٓـُٔواْ بِمَا عَمِلُواْ وَيَجۡزِيَ ٱلَّذِينَ أَحۡسَنُواْ بِٱلۡحُسۡنَى ﴾
[النَّجم: 31]
﴿ولله ما في السموات وما في الأرض ليجزي الذين أساءوا بما عملوا﴾ [النَّجم: 31]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo zonse za kumwamba ndi zadziko lapansi nza Allah Yekha, (pozilenga ndi kuziyang’anira), kuti adzawalipire amene adaipitsa pa zimene adachita ndi kutinso adzawalipire zabwino amene adachita zabwino |