×

Ndithudi Mulungu wamva mau a mkazi amene ali kutsutsana ndi iwe pa 58:1 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mujadilah ⮕ (58:1) ayat 1 in Chichewa

58:1 Surah Al-Mujadilah ayat 1 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mujadilah ayat 1 - المُجَادلة - Page - Juz 28

﴿قَدۡ سَمِعَ ٱللَّهُ قَوۡلَ ٱلَّتِي تُجَٰدِلُكَ فِي زَوۡجِهَا وَتَشۡتَكِيٓ إِلَى ٱللَّهِ وَٱللَّهُ يَسۡمَعُ تَحَاوُرَكُمَآۚ إِنَّ ٱللَّهَ سَمِيعُۢ بَصِيرٌ ﴾
[المُجَادلة: 1]

Ndithudi Mulungu wamva mau a mkazi amene ali kutsutsana ndi iwe pa nkhani ya mwamuna wake ndipo iye wapereka madandaulo ake kwa Mulungu. Ndipo Mulungu wamva kukangana kwanu chifukwa Iye amamva ndiponso amaona chili chonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قد سمع الله قول التي تجادلك في زوجها وتشتكي إلى الله والله, باللغة نيانجا

﴿قد سمع الله قول التي تجادلك في زوجها وتشتكي إلى الله والله﴾ [المُجَادلة: 1]

Khaled Ibrahim Betala
“۞ Ndithu Allah wamva mawu a (mkazi) amene akubwezeranabwezerana nawe (mawu) pa za mwamuna wake (amene adamsala); ndipo akusuma kwa Allah. Ndipo Allah akumva kukambirana kwanu; ndithu Allah Ngwakumva, Ngopenya (chilichonse)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek