×

Motero mapeto awo ndi akuti onsewa adzapsa ku moto kumene adzakhalako mpaka 59:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:17) ayat 17 in Chichewa

59:17 Surah Al-hashr ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 17 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿فَكَانَ عَٰقِبَتَهُمَآ أَنَّهُمَا فِي ٱلنَّارِ خَٰلِدَيۡنِ فِيهَاۚ وَذَٰلِكَ جَزَٰٓؤُاْ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الحَشر: 17]

Motero mapeto awo ndi akuti onsewa adzapsa ku moto kumene adzakhalako mpaka kalekale. Limenelo ndilo dipo la anthu ochita zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فكان عاقبتهما أنهما في النار خالدين فيها وذلك جزاء الظالمين, باللغة نيانجا

﴿فكان عاقبتهما أنهما في النار خالدين فيها وذلك جزاء الظالمين﴾ [الحَشر: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho mapeto a onse awiriwo, kudali kukalowa ku Moto ndi kukhala m’menemo nthawi yaitali. Iyi ndiyo mphoto ya anthu onyenga (ochenjelera anzawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek