Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 147 - الأنعَام - Page - Juz 8
﴿فَإِن كَذَّبُوكَ فَقُل رَّبُّكُمۡ ذُو رَحۡمَةٖ وَٰسِعَةٖ وَلَا يُرَدُّ بَأۡسُهُۥ عَنِ ٱلۡقَوۡمِ ٱلۡمُجۡرِمِينَ ﴾
[الأنعَام: 147]
﴿فإن كذبوك فقل ربكم ذو رحمة واسعة ولا يرد بأسه عن القوم﴾ [الأنعَام: 147]
Khaled Ibrahim Betala “Ngati akukutsutsa (pa zimene zavumbulutsidwa), auze (mowachenjeza): “Mbuye wanu (Yemwe ngofunika kum’khulupirira ndi kutsatira malamulo ake) Ngwachifundo chambiri (kwa yemwe akumumvera, ndi yemwe akumunyoza pano pa dziko lapansi). Komatu chilango chake sichibwezedwa kwa anthu oipa.” |